Machitidwe 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo anagwa pansi ndipo anamva mawu akumuuza kuti: “Saulo, Saulo n’chifukwa chiyani ukundizunza?”+ Machitidwe 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinagwa pansi ndi kumva mawu akuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza?’+
4 Pamenepo anagwa pansi ndipo anamva mawu akumuuza kuti: “Saulo, Saulo n’chifukwa chiyani ukundizunza?”+