Numeri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu anauza Balamu kuti: “Usapite nawo, ndipo anthuwo usakawatemberere,+ pakuti iwo ndi odalitsidwa.”+ Numeri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Balaki anapsera mtima Balamu n’kuwomba m’manja.+ Kenako anauza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere+ adani anga, koma iwe wawadalitsa kwambiri katatu konseka!
12 Koma Mulungu anauza Balamu kuti: “Usapite nawo, ndipo anthuwo usakawatemberere,+ pakuti iwo ndi odalitsidwa.”+
10 Pamenepo Balaki anapsera mtima Balamu n’kuwomba m’manja.+ Kenako anauza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere+ adani anga, koma iwe wawadalitsa kwambiri katatu konseka!