Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ine ndidzatulutsa mtundu waukulu mwa iwe. Ndidzakudalitsa ndi kukuza dzina lako, ndipo iwe ukhale dalitso+ kwa ena.

  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+

  • Numeri 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inetu ndalamulidwa kudzadalitsa,

      Ndipo Iye wadalitsa,+ ine sindisintha zimenezo.+

  • Deuteronomo 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yehova Mulungu wanu sanafune kumvera Balamu,+ m’malomwake Yehova Mulungu wanu anakusinthirani temberero kukhala dalitso,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu anakukondani.+

  • Deuteronomo 33:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiwe wodala Isiraeli iwe!+

      Ndani angafanane ndi iwe,+

      Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+

      Chishango chako chokuthandiza,+

      Amenenso ndi lupanga lako lopambana?+

      Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+

      Ndipo iwe udzayendayenda pamalo awo okwezeka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena