Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Isiraeli, khulupirira Yehova.+Iye ndiye thandizo lako ndi chishango chako.+
15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+