Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiwe wodala Isiraeli iwe!+

      Ndani angafanane ndi iwe,+

      Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+

      Chishango chako chokuthandiza,+

      Amenenso ndi lupanga lako lopambana?+

      Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+

      Ndipo iwe udzayendayenda pamalo awo okwezeka.”+

  • Salimo 33:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+

      Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+

  • Salimo 119:114
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 114 Inu ndinu malo anga obisalamo ndi chishango changa,+

      Pakuti ndayembekezera mawu anu.+

  • Salimo 144:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+

      Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+

      Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+

      Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+

  • Miyambo 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mawu alionse a Mulungu ndi oyera.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena