Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+ Salimo 144:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+ Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+
5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+