Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+ Salimo 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Salimo 144:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+