Yoswa 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+ Yeremiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+
19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+