Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse,+ chifukwatu mtundu wanu unali waung’ono mwa mitundu yonse.+

  • Deuteronomo 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye analinso kukonda anthu ake.+

      Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+

      Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+

      Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+

  • Ezekieli 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Ndinadutsa pafupi nawe n’kukuona, ndipo ndinaona kuti inali nthawi yako yoti uchite zachikondi.+ Chotero ndinakuphimba ndi chovala changa+ ndipo ndinabisa maliseche ako. Ndinakulumbirira n’kuchita nawe pangano+ ndipo unakhala wanga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Malaki 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova wanena kuti: “Ine ndimakukondani anthu inu.”+

      Koma inu mwanena kuti: “Mumatikonda motani?”+

      “Kodi Esau sanali m’bale wake wa Yakobo?+ Koma ine ndinakonda Yakobo,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena