-
Yeremiya 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Pita, ukafuule m’makutu a anthu a ku Yerusalemu kuti, ‘Yehova wanena kuti:+ “Ndikukumbukira bwino kwambiri kukoma mtima kosatha kumene unali nako pamene unali wachinyamata,+ chikondi chimene unali nacho pa nthawi imene unali kulonjezedwa kukwatiwa,+ ndi kuti unanditsatira poyenda m’chipululu, m’dziko losabzalidwa kalikonse.+
-