Deuteronomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene dzanja lanu likuchita.+ Iye akudziwa za kuyenda kwanu kudutsa m’chipululu chachikulu ichi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi,+ ndipo simunasowe kanthu.”’+ Nehemiya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.
7 Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene dzanja lanu likuchita.+ Iye akudziwa za kuyenda kwanu kudutsa m’chipululu chachikulu ichi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi,+ ndipo simunasowe kanthu.”’+
12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.