Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kwa zaka 40+ munawapatsa chakudya m’chipululu. Iwo sanasowe kanthu.+ Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.+

  • Salimo 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova ndi M’busa wanga.+

      Sindidzasowa kanthu.+

  • Salimo 34:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Opani Yehova, inu oyera ake,+

      Pakuti onse omuopa sasowa kanthu.+

  • Salimo 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+

      Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+

  • Salimo 37:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+

      Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+

      Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+

  • Afilipi 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nayenso Mulungu wanga+ adzakupatsani zosowa zanu zonse+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake+ chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena