Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+ Salimo 105:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mulungu anayala mtambo kuti uziwatchinga,+Ndipo anawapatsa moto kuti uziwaunikira usiku.+
14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+