Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Salimo 105:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Wakumbukira lonjezo limene anapereka ku mibadwo 1,000,+ Luka 1:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+
42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.
8 Wakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Wakumbukira lonjezo limene anapereka ku mibadwo 1,000,+ Luka 1:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+