Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.

  • Ekisodo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+

  • Deuteronomo 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira.

  • Salimo 106:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+

      Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Luka 1:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena