Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+
34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+