Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ Deuteronomo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo tinayamba kufuulira Yehova Mulungu wa makolo athu,+ ndipo Yehova anamva mawu athu+ ndi kuona nsautso yathu, mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu.+
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+
7 Pamenepo tinayamba kufuulira Yehova Mulungu wa makolo athu,+ ndipo Yehova anamva mawu athu+ ndi kuona nsautso yathu, mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu.+