Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*

  • Ekisodo 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Motero ineyo ndamva kubuula kwa ana a Isiraeli,+ amene Aiguputo akuwagwiritsa ntchito yaukapolo, ndipo ndikukumbukira pangano langa.+

  • Salimo 106:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Mulungu akamva kuchonderera kwawo+

      Anali kuona kuvutika kwawo.+

  • Yesaya 63:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+

  • Machitidwe 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena