Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+

  • Ekisodo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+

  • Numeri 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Paja kale makolo athu anapita ku Iguputo,+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.+ Aiguputowo anatizunza ife ndi makolo athu.+

  • Deuteronomo 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo Aiguputo anayamba kutichitira zoipa, kutizunza ndi kutigwiritsa ntchito yowawa yaukapolo.+

  • Machitidwe 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena