Deuteronomo 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse, Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+
18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse,