Deuteronomo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Cholinga chake n’chakuti akukhazikitseni lero monga anthu ake+ ndi kuti akuonetseni kuti ndi Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani ndiponso monga mmene analumbirira makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+
13 Cholinga chake n’chakuti akukhazikitseni lero monga anthu ake+ ndi kuti akuonetseni kuti ndi Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani ndiponso monga mmene analumbirira makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+