Rute 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+ 1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+ Yesaya 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndakutenga kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+ ndiponso ndakuitana kuchokera kumadera akutali a dziko lapansi.+ Chotero ndinakuuza kuti, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga.+ Ndasankha iweyo+ ndipo sindinakutaye.+
9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
9 Ndakutenga kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+ ndiponso ndakuitana kuchokera kumadera akutali a dziko lapansi.+ Chotero ndinakuuza kuti, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga.+ Ndasankha iweyo+ ndipo sindinakutaye.+