Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+

  • Salimo 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Amatsitsimula moyo wanga.+

      Amanditsogolera m’tinjira tachilungamo chifukwa cha dzina lake.+

  • Salimo 106:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+

      Kuti mphamvu zake zidziwike.+

  • Yeremiya 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+

  • Ezekieli 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa mitundu ya anthu amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena