1 Mafumu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzakhaladi pakati pa ana a Isiraeli,+ ndipo sindidzasiya anthu anga, Aisiraeli.”+ Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+ Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+