1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+ Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+