Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu. Paja inenso ndine mmodzi wa Aisiraeli, mbadwa* ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu. Paja inenso ndine mmodzi wa Aisiraeli, mbadwa* ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.