Yobu 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu adzamuwombera m’manja monyoza.+Ndipo adzamuimbira mluzu+ ali pamalo pake. Nahumu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Masoka ako sadzakupatsa mpata wopuma. Chilonda chako chakhala chosachiritsika.+ Kodi pali amene sunamuvutitse ndi zoipa zako nthawi zonse?+ N’chifukwa chake onse amene adzamva za iwe adzakuwombera m’manja.”+
19 Masoka ako sadzakupatsa mpata wopuma. Chilonda chako chakhala chosachiritsika.+ Kodi pali amene sunamuvutitse ndi zoipa zako nthawi zonse?+ N’chifukwa chake onse amene adzamva za iwe adzakuwombera m’manja.”+