Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Balaki anapsera mtima Balamu n’kuwomba m’manja.+ Kenako anauza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere+ adani anga, koma iwe wawadalitsa kwambiri katatu konseka!

  • Maliro 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anthu onse odutsa mumsewu akakuona, akuwomba m’manja+ monyodola.

      Akuimba mluzu+ ndi kupukusa mitu+ yawo poona mwana wamkazi wa Yerusalemu. Iwo akunena kuti:

      “Kodi uwu ndi mzinda umene anali kunena kuti, ‘Ndi wokongola kwambiri, wotamandika padziko lonse lapansi’?”+

  • Nahumu 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Masoka ako sadzakupatsa mpata wopuma. Chilonda chako chakhala chosachiritsika.+ Kodi pali amene sunamuvutitse ndi zoipa zako nthawi zonse?+ N’chifukwa chake onse amene adzamva za iwe adzakuwombera m’manja.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena