Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu wawala ali ku Ziyoni,+ mzinda wokongola kwambiri.+ Ezekieli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Dzina lako linatchuka pakati pa mitundu ya anthu chifukwa cha kukongola kwako, pakuti linali labwino kwambiri chifukwa cha ulemerero wanga umene ndinaika pa iwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+
14 “‘Dzina lako linatchuka pakati pa mitundu ya anthu chifukwa cha kukongola kwako, pakuti linali labwino kwambiri chifukwa cha ulemerero wanga umene ndinaika pa iwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”