Salimo 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu wakhala mfumu ya mitundu ya anthu.+Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika.+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Mateyu 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kapena kutchula dziko lapansi chifukwa ndi chopondapo mapazi ake,+ kapena kutchula Yerusalemu chifukwa ndi mzinda+ wa Mfumu yaikulu.
35 kapena kutchula dziko lapansi chifukwa ndi chopondapo mapazi ake,+ kapena kutchula Yerusalemu chifukwa ndi mzinda+ wa Mfumu yaikulu.