Salimo 76:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo ake opumulirako ali ku Salemu,+Malo ake okhalamo ali ku Ziyoni.+ Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene analikonda.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+ Salimo 134:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova, amene ndiye Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Akudalitseni ali ku Ziyoni.+