Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+

      Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+

      Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+

  • Salimo 20:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Atumize thandizo kuchokera kumalo oyera.+

      Akuchirikizeni ali ku Ziyoni.+

  • Salimo 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mulungu wawala ali ku Ziyoni,+ mzinda wokongola kwambiri.+

  • Salimo 128:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova adzakudalitsa ali ku Ziyoni.+

      Komanso usangalale ndi zinthu zabwino za mu Yerusalemu masiku onse a moyo wako,+

  • Aroma 11:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena