Genesis 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Aheberi 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Melekizedeki ameneyu, mfumu ya mzinda wa Salemu, analinso wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Iyeyu ndi amene anachingamira Abulahamu pochokera kokagonjetsa mafumu, ndipo anamudalitsa.+
18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+
7 Melekizedeki ameneyu, mfumu ya mzinda wa Salemu, analinso wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Iyeyu ndi amene anachingamira Abulahamu pochokera kokagonjetsa mafumu, ndipo anamudalitsa.+