Aheberi 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Melekizedeki ameneyu, mfumu ya mzinda wa Salemu, analinso wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Iyeyu ndi amene anachingamira Abulahamu pochokera kokagonjetsa mafumu, ndipo anamudalitsa.+
7 Melekizedeki ameneyu, mfumu ya mzinda wa Salemu, analinso wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+ Iyeyu ndi amene anachingamira Abulahamu pochokera kokagonjetsa mafumu, ndipo anamudalitsa.+