Aheberi 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Melekizedeki ameneyu anali mfumu ya mzinda wa Salemu komanso wansembe wa Mulungu Wamʼmwambamwamba, ndipo anachingamira Abulahamu pochokera kokapha mafumu nʼkumudalitsa.+
7 Melekizedeki ameneyu anali mfumu ya mzinda wa Salemu komanso wansembe wa Mulungu Wamʼmwambamwamba, ndipo anachingamira Abulahamu pochokera kokapha mafumu nʼkumudalitsa.+