Salimo 110:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+ Aheberi 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kumene Yesu, yemwe ndi kalambulabwalo anakalowa chifukwa cha ife.+ Iyeyu wakhala mkulu wa ansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+ Aheberi 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Popeza kuti analibe bambo, analibe mayi, analibe mzere wa mibadwo ya makolo ndipo tsiku limene anabadwa+ komanso limene anamwalira silikudziwika, koma anamuchititsa kuti afanane ndi Mwana wa Mulungu,+ iye ndi wansembe kwamuyaya.+ Aheberi 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Izi zinachitika m’njira yakuti iye anali adakali m’chiuno+ mwa kholo lake pamene Melekizedeki anakumana ndi kholo lakelo.+
4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+
20 kumene Yesu, yemwe ndi kalambulabwalo anakalowa chifukwa cha ife.+ Iyeyu wakhala mkulu wa ansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+
3 Popeza kuti analibe bambo, analibe mayi, analibe mzere wa mibadwo ya makolo ndipo tsiku limene anabadwa+ komanso limene anamwalira silikudziwika, koma anamuchititsa kuti afanane ndi Mwana wa Mulungu,+ iye ndi wansembe kwamuyaya.+
10 Izi zinachitika m’njira yakuti iye anali adakali m’chiuno+ mwa kholo lake pamene Melekizedeki anakumana ndi kholo lakelo.+