Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yosefe anali kale ku Iguputo.+ Anthu onse otuluka m’chiuno mwa Yakobo+ analipo 70. Aroma 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinalitu wamoyo chilamulo chisanabwere.+ Koma pamene malamulo anafika,+ uchimo unakhalanso ndi moyo, koma ineyo ndinafa.+
9 Ndinalitu wamoyo chilamulo chisanabwere.+ Koma pamene malamulo anafika,+ uchimo unakhalanso ndi moyo, koma ineyo ndinafa.+