Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+ Aheberi 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Izi zinachitika m’njira yakuti iye anali adakali m’chiuno+ mwa kholo lake pamene Melekizedeki anakumana ndi kholo lakelo.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
10 Izi zinachitika m’njira yakuti iye anali adakali m’chiuno+ mwa kholo lake pamene Melekizedeki anakumana ndi kholo lakelo.+