Salimo 87:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova amakonda kwambiri zipata za Ziyoni+Kusiyana ndi mahema onse a Yakobo.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+Tamandani Ya, anthu inu!+