Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kumwamba kukondwere, ndipo dziko lapansi lisangalale,+

      Ndipo anene pakati pa anthu a mitundu ina kuti: ‘Yehova wakhala mfumu!’+

  • Salimo 96:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+

      Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+

      Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+

  • Salimo 97:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+

      Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+

  • Chivumbulutso 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena