Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Salimo 44:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+ Mateyu 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano anthu odutsa anayamba kunena mawu onyoza+ Yesu. Anali kupukusa+ mitu yawo Maliko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+
29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+