Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kwa iwo ndakhala chinthu choyenera kutonzedwa.+Akandiona amapukusa mitu yawo.+ Luka 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
35 Anthu anangoima chilili kuonerera zochitikazo.+ Koma olamulira anali kumunyogodola kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, m’lekeni adzipulumutse yekha,+ ngati iyeyu alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+