Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kwa iwo ndakhala chinthu choyenera kutonzedwa.+Akandiona amapukusa mitu yawo.+ Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+