Salimo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anditsegulira pakamwa pawo mondiopseza,+Ngati mkango wokhadzula nyama umenenso ukubangula.+ Zekariya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma.+ Zimenezi ndi ndalama za mtengo wapatali zimene akuona kuti angandigule nazo.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo n’kukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
13 Zitatero Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma.+ Zimenezi ndi ndalama za mtengo wapatali zimene akuona kuti angandigule nazo.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo n’kukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+