Machitidwe 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+ Machitidwe 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mulungu wa makolo athu anaukitsa+ Yesu, amene inu munamupha mwa kumupachika pamtengo.+
23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+