Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Mika 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+ Mateyu 26:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Kenako anayamba kumulavulira kunkhope+ ndi kum’menya+ nkhonya. Ena anamuwomba mbama,+ Yohane 6:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+
66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+