Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+ Yohane 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+
3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+