Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:3 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,2/2017, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 268/1/2000, tsa. 32 Yesaya 2, ptsa. 200-202
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+
53:3 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,2/2017, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 268/1/2000, tsa. 32 Yesaya 2, ptsa. 200-202