Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma. Zimenezi ndi ndalama zochepa zimene aona kuti angandilipire.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo nʼkukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+

  • Yohane 18:39, 40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Pajanso inu muli ndi mwambo wakuti ndizikumasulirani munthu mmodzi pa Pasika.+ Ndiye kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayuda?” 40 Anthuwo anafuulanso kuti: “Ameneyo ayi, koma Baraba!” Komatu Baraba ameneyu anali wachifwamba.+

  • Machitidwe 3:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula. 14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo, ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wopha anthu.+

  • Machitidwe 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yesu ameneyu ndi ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena