Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 118:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana

      Wakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+

  • Yesaya 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Ndikuika mwala woyesedwa mu Ziyoni kuti ukhale maziko,+

      Umenewu ndi mwala wapakona wamtengo wapatali+ wa maziko olimba.+

      Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+

  • Mateyu 21:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ?

  • 1 Petulo 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa mumamukhulupirira. Koma kwa amene samukhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena